top of page
Kumwamba kapena Kuuka   

 

Mulungu sanatilonjeze kuti tikupita kumwamba, palibe vesi limodzi m’Baibulo lofotokoza “kupita kumwamba”. Iye anati,

  • YOHANE 3:13 Palibe munthu anakwera Kumwamba, koma Iye wotsikayo kuchokera Kumwamba, ndiye Mwana wa munthu wa Kumwambayo.

  • Machitidwe a Atumwi 2:29 “Amuna inu, abale, lolani ndinene kwa inu momasuka za kholo lakale Davide, kuti anamwalira ndipo anaikidwa m’manda, ndipo manda ake ali ndi ife mpaka lero. 30 Chifukwa chake pokhala mneneri, ndipo podziwa kuti Mulungu adalumbirira ndi lumbiro kwa iye, kuti mwa chipatso cha thupi lake, monga mwa thupi, adzaukitsa Khristu kukhala pa mpando wake wachifumu; za kuuka kwa Kristu, kuti moyo wake sunasiyidwa m’Hade, kapena thupi lake silinaona chibvundi. 32 Yesu ameneyo Mulungu anamuukitsa, za ichi tiri mboni ife tonse. 33 Chifukwa chake atakwezedwa kudzanja lamanja la Mulungu, nalandira kwa Atate lonjezano la Mzimu Woyera, anatsanulira ichi chimene inu muchiona ndi kumva tsopano.34 Pakuti Davide sanakwere kumwamba, koma iye mwini anati: Ambuye anati kwa Ambuye wanga, Khala pa dzanja langa lamanja,

Mavesi ali m’munsiwa akufotokoza kuti tikamwalira, timapita kumanda n’kumayembekezera chiukiriro. ● Yohane 5:28 Musazizwe ndi ichi; pakuti ikudza nthawi, imene onse ali m’manda adzamva mawu ake. 29 Ndipo adzatuluka;

  • Chivumbulutso 20:4 Kenako ndinaona mipando yachifumu, ndipo amene anakhalapo anapatsidwa ulamuliro woweruza. Ndipo ndinaona mizimu ya iwo amene adadulidwa mitu chifukwa cha umboni wa Yesu, ndi chifukwa cha mawu a Mulungu, ndi iwo amene sanapembedze chilombo kapena fano lake, ndipo sanalandire chizindikiro pamphumi pawo kapena m'manja mwawo. Ndipo anakhala ndi moyo, nalamulira pamodzi ndi Kristu zaka chikwi.

  • Chivumbulutso 20:5 Otsala a akufawo sanakhalenso ndi moyo kufikira zitatha zaka 1,000. Ichi ndi kuuka koyamba.

  • Chibvumbulutso 20:6 Wodala ndi woyera mtima ali iye amene achita nawo pa kuuka koyamba; pa iwowa imfa yachiwiri ilibe mphamvu; koma adzakhala ansembe a Mulungu ndi a Kristu, nadzachita ufumu pamodzi ndi Iye zaka chikwi.

  • Yohane 5:24 “Indetu, indetu, ndinena kwa inu, Iye wakumva mawu anga, ndi kukhulupirira Iye amene anandituma Ine, ali nawo moyo wosatha; 25 Indetu, indetu, ndinena kwa inu, ikudza nthawi, ndipo ilipo tsopano, imene akufa adzamva mawu a Mwana wa Mulungu; ndipo amene amva adzakhala ndi moyo. 26 Pakuti monga Atate ali ndi moyo mwa Iye yekha, momwemonso anapatsa Mwana kukhala ndi moyo mwa Iye yekha;

27 Ndipo adampatsa Iye mphamvu yakuweruza, chifukwa ndiye Mwana wa

Munthu. 28 Musazizwe ndi ichi; pakuti ikudza nthawi, imene onse ali m’manda adzamva mawu ake. 29 Ndipo adzatuluka; 30 Ine sindingathe kuchita kanthu mwa Ine ndekha. monga ndimva, ndiweruza; ndipo chiweruzo changa chiri cholungama, chifukwa sinditsata chifuniro changa, koma chifuniro cha Atate wondituma Ine.

 

  • Danieli 12:2 Ndipo ambiri mwa iwo amene agona m’fumbi lapansi adzauka, ena kumoyo wosatha, ena ku manyazi ndi mnyozo wosatha.3 Anthu anzeru adzawala.

  • Yohane 11:23 Yesu anati kwa iye, “Mlongo wako adzaukanso.” 24 Marita anati kwa Iye,

“Ndidziwa kuti adzauka pa kuuka kwa akufa m’tsiku lotsiriza.” Yesu anati kwa iye, “Ine ndine kuuka ndi moyo. Wokhulupirira Ine, angakhale amwalira, adzakhala ndi moyo. 26 Ndipo yense wakukhala ndi moyo, nakhulupirira Ine, sadzamwalira nthawi yonse. Kodi mukukhulupirira izi?”

  • Act 4:1 Ndipo m’mene adalikuyankhula ndi anthu, ansembe ndi mdindo wa Kachisi ndi Asaduki adadza kwa iwo, 2 nabvutika mtima chifukwa adaphunzitsa anthu, nalalikira mwa Yesu za kuwuka kwa akufa.

  • Machitidwe a Atumwi 23:6 Koma pamene Paulo anazindikira kuti gulu lina linali la Asaduki, ndipo linalo linali la Afarisi, anafuula m’bwalo la akulu kuti: “Amuna inu, abale, ine ndine Mfarisi, mwana wa Mfarisi; za chiyembekezo ndi kuuka kwa akufa ndikuweruzidwa. ● Machitidwe 24:15-16 Ndikhala nacho chiyembekezo mwa Mulungu, chimene iwonso avomereza, kuti kudzakhala kuuka kwa akufa, olungama ndi osalungama; 16 Potero, ine ndekha ndiyesetsa nthawi zonse kukhala ndi chikumbumtima chosandikhumudwitsa kwa Mulungu ndi kwa anthu. ● 1 Atesalonika 4:13-18 Koma sindifuna kuti mukhale osadziwa, abale, za iwo akugona, kuti mungalire, monganso enawo amene alibe chiyembekezo. 14 Pakuti popeza tikhulupirira kuti Yesu adamwalira, nauka, tikhulupiriranso kuti Yehova adzatenga pamodzi ndi Yesu iwo akugona mwa Iye. 15 Pakuti ichi tikunena kwa inu m'mawu a Ambuye, kuti ife okhala ndi moyo, otsalira kufikira kufikapo kwa Ambuye, sitidzatsogolera iwo akugonawo. liwu la mngelo wamkulu ndi lipenga la Mulungu, ndipo akufa mwa Khristu adzayamba kuwuka. 17) Pamenepo ife okhala ndi moyo, otsalafe, tidzakwatulidwa nawo pamodzi m’mitambo, kukakomana ndi Ambuye mumlengalenga; 18 Chifukwa chake tonthozanani wina ndi mzake ndi mawu awa.

no one has gone to Heaven except those who came down

What did Jesus say about a man going to heaven? John 3:13 And no man hath ascended up to heaven, but he that came down from heaven, even the Son of man which is in heaven.

Is King David, a man after God’s heart, in heaven? Acts 2:34 For David is not ascended into the heavens...

Is King David still in the grave? Acts 2:29 Men and brethren, let me freely speak unto you of the patriarch David, that he is both dead and buried, and his sepulcher is with us unto this day

What did Jesus say about those dead in the grave? John 5:28 Marvel not at this: for the hour is coming, in the which all that are in the graves shall hear his voice.

What did Jesus call this event when all that are dead would hear His voice? John 5:29 and shall come forth; they that have done good, unto the resurrection of life; and they that have done evil, unto the resurrection of judgment. (ASV)

At the resurrection, will you live forever? Luke 20:36 Neither can they die anymore: for they are equal unto the angels; and are the children of God, being the children of the resurrection.


 

bottom of page