top of page

 

Yeshua Akulankhula za Tsogolo.Palibe mkwatulo wachinsinsi! 

 

 (Palibe mkwatulo wachinsinsi; Akhristu amaphunzitsidwa kuti ndi chinsinsi sichipezeka mu bible. Mkwatulo uwu ndi wa Akhristu okha, Ayuda adzasiyidwa kuti adutse chisautso .) 

   Mateyu 24:

Mukakhala pa njira ya chipulumutso mwamezetsanidwa mu Israeli ndinu Myuda wauzimu. Ayi, Myuda weniweni ndi munthu amene mtima wake uli wolungama pamaso pa Mulungu. Ndipo mdulidwe weniweni suli kungotsatira zolembedwa za lamulo; koma ndi kusintha kwa mtima komwe kumapangidwa ndi Mzimu. Ndipo munthu wosintha mtima amafuna kutamandidwa ndi Mulungu, osati kwa anthu. Aroma 2:29 Kodi chizindikiro cha kubweranso kwanu ndi kutha kwa dziko lapansi ndi chiyani?

  1. Chiyambi cha zowawa.

  2. Mukadzawona chonyansa cha kupululutsa,

  3. “Pamenepo amene ali mu Yudeya athawire kumapiri.

  4. Paskha

  5. Sukkot

  6. Greater eksodo

  7. pamenepo adzakuperekani kunsautso, nadzakuphani;

  8.  Pamenepo padzakhala chisautso chachikulu

  9.  Pakuti akhristu onyenga ndi aneneri onyenga adzawuka nadzawonetsa zizindikiro zazikulu ndi zozizwa.
    kunyenga,

  10. Koma iye wakulimbika chilimbikire kufikira kuchimaliziro, ndiye amene adzapulumuka.

  11. “Pomwepo pambuyo pa chisautso cha masiku amenewo, dzuŵa lidzadetsedwa, ndi mwezi sudzapereka kuwala kwake; nyenyezi zidzagwa kuchokera kumwamba, ndi mphamvu zakumwamba zidzagwedezeka. 30 Kenako chizindikiro cha Mwana wa Munthu chidzaonekera kumwamba.

  12. Mkwiyo wa Mulungu

  

 

Yesu Ananeneratu za kuwonongedwa kwa Kachisi

24 Pamenepo Yesu anaturuka nachoka m’Kachisi, ndipo ophunzira ake anadza kudzamuwonetsa nyumba za Kachisiyo. 2 Ndipo Yesu anati kwa iwo, Kodi simukuziwona zonsezi? Indetu, ndinena kwa inu, palibe mwala umodzi udzasiyidwa pano pamwamba pa umzake, umene sudzagwetsedwa pansi.

Zizindikiro za Nthawi ndi Mapeto a M'badwo

3 Tsopano pamene Iye analikukhala pa Phiri la Azitona, ophunzira anadza kwa Iye mwamseri, nanena, “Tiuzeni, kodi zimenezi zidzachitika liti? Ndipo chizindikiro cha kufika kwanu nchiyani, ndi cha mathedwe a nthawi ya pansi pano?

4 Ndipo Yesu anawayankha kuti: “Samalani kuti munthu asakunyengeni. 5 Pakuti ambiri adzabwera m’dzina langa ndi kunena kuti, ‘Ine ndine Khristu,’ + ndipo adzasocheretsa anthu ambiri. 6 Ndipo mudzamva za nkhondo ndi mbiri za nkhondo; Penyani kuti musade nkhawa; za [a]zinthu zonsezi ziyenera kuchitika, koma chitsiriziro sichinafike. 7 Pakuti mtundu udzaukirana ndi mtundu wina, ndi ufumu ndi ufumu wina. ndipo padzakhala njala, [b]miliri ndi zivomezi m’malo akutiakuti. 8 Zonsezi ndi chiyambi cha zowawa.

9 “Pamenepo adzakuperekani ku chisautso ndi kukuphani, ndipo anthu a mitundu yonse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa. 10 Ndipo pamenepo ambiri adzakhumudwa, nadzaperekana wina ndi mzake, nadzadana wina ndi mzake. 11 Pamenepo adzauka aneneri onyenga ambiri, nadzasokeretsa ambiri. 12 Ndipo chifukwa cha kuchuluka kwa kusayeruzika, chikondi cha anthu ambiri chidzazirala. 13 Koma iye wakulimbika chilimbikire kufikira kuchimaliziro, ndiye amene adzapulumuka. 14 Ndipo uthenga uwu wabwino wa Ufumu udzalalikidwa padziko lonse lapansi, ukhale mboni kwa anthu a mitundu yonse; ndipo pomwepo chidzafika chimaliziro.

Chisautso Chachikulu

15 “Chotero mukadzaona ‘chonyansa cha kupululutsa,’ chimene chinanenedwa ndi mneneri Danieli, chitaima m’malo oyera, + (amene aŵerenga azindikire), 16pamenepo iwo ali mu Yudeya athawire kumapiri.17 Iye amene ali padenga la nyumba asatsike kukatenga chilichonse m’nyumba mwake. 18 Ndipo iye amene ali kumunda asabwerere kukatenga zobvala zake. 19 Koma tsoka kwa iwo akukhala ndi pakati ndi akuyamwitsa m’masiku amenewo! 20 Ndipo pempherani kuti kuthawa kwanu kusakhale pa nyengo yachisanu, kapena pa Sabata; 21 Pakuti pamenepo padzakhala masautso akulu, monga sipadakhale otero kuyambira chiyambi cha dziko kufikira tsopano, inde, ndipo sipadzakhalanso. 22 Ndipo akadapanda kufupikitsidwa masikuwo, sakadapulumuka munthu aliyense; koma kwa [c]chifukwa cha osankhidwawo, masiku awo adzafupikitsidwa.

23 “Pamenepo wina akadzakuuzani kuti, 'Onani, Khristu ali kuno!' kapena 'Uko!' musakhulupirire. 24 Pakuti Akhristu onyenga adzawuka, ndi aneneri onyenga nadzawonetsa zizindikiro zazikulu ndi zodabwitsa kuti akanyenge, ngati n’kotheka, osankhidwa omwe. 25 Onani, ndakuwuzanitu kale.

26 “Chotero akanena kwa inu, Onani, ali m’chipululu; musatuluke; kapena, Taonani, ali m'zipinda; musakhulupirire. 27 Pakuti monga mphezi idzera kum’mawa, niwonekera kumadzulo, kotero kudzakhala kufika kwa Mwana wa munthu. 28 Pakuti kumene kuli mtembo, miimba idzasonkhana komweko.

Kubwera kwa Mwana wa Munthu

29“Pomwepo pambuyo pa chisautso cha masiku amenewo, dzuŵa lidzadetsedwa, ndi mwezi sudzapereka kuwala kwake; nyenyezi zidzagwa kuchokera kumwamba, ndi mphamvu zakumwamba zidzagwedezeka. 30Kenako chizindikiro cha Mwana wa munthu chidzaonekera kumwamba.+ Kenako mafuko onse a padziko lapansi adzadziguguda pachifuwa, + ndipo adzaona Mwana wa munthu akubwera pamitambo yakumwamba ndi mphamvu ndi ulemerero waukulu. 31 Ndipo Iye adzatumiza angelo ake ndi kulira kwamphamvu kwa lipenga, ndipo iwo adzasonkhanitsa ake.d]osankhidwa kuchokera ku mphepo zinayi, kuchokera ku malekezero akumwamba kufikira malekezero ena.

Fanizo la Mtengo wa Mkuyu

32 “Tsopano phunzirani fanizo ili pa mtengo wa mkuyu: Nthambi yake ikayamba kukhala yanthete n’kuphuka masamba, mumadziwa kuti dzinja lili pafupi. 33 Chotero inunso, pamene muwona zinthu zonsezi, zindikirani kuti . . .e] chiri pafupi—pamakomo! 34 Indetu, ndinena kwa inu, mbadwo uwu sudzatha kuchoka kufikira zinthu zonsezi zitachitika. 35 Thambo ndi dziko lapansi zidzapita, koma mawu anga sadzapita.

Palibe Amene Akudziwa Tsiku Kapena Ola

36 “Koma za tsikulo ndi nthawi yake palibe amene akudziwa, ngakhale angelof]kumwamba, koma Atate Anga okha. 37 Koma monga anali masiku a Nowa, kotero kudzakhala kufika kwake kwa Mwana wa munthu. 38 Pakuti monga m’masiku aja, chisanafike chigumula, anthu anali kudya ndi kumwa, kukwatira ndi kukwatiwa, kufikira tsiku limene Nowa analowa m’chingalawa; kudza kwa Mwana wa Munthu kukhale. 40 Pomwepo adzakhala awiri m’munda: m’modzi adzatengedwa, ndi wina adzasiyidwa. 41 Akazi awiri adzakhala akupera pamphero: m’modzi adzatengedwa, ndi wina adzasiyidwa. 42 Chifukwa chake dikirani, pakuti simudziwa chimeneg]nthawi yakudza Ambuye wanu. 43 Koma dziwani ichi, kuti mwini nyumba akadadziwa chimeneh]nthawi ikafika mbala, akadadikira, osalola kuti nyumba yake ithyoledwe. 44 Chifukwa chake khalani inunso okonzekeratu; pakuti Mwana wa munthu adzadza pa ola limene simukuliyembekezera.

Kapolo Wokhulupirika ndi Kapolo Woipayo

45“Ndani tsono amene ali kapolo wokhulupirika ndi wanzeru, amene mbuye wake anamuika kukhala woyang’anira banja lake, kuwapatsa chakudya?ndi]nthawi yake? 46 Wodala kapolo amene mbuye wake, pakufika, adzampeza akuchita chotero. 47 Indetu, ndinena kwa inu, kuti adzamkhazika iye wolamulira zinthu zake zonse. 48 Koma ngati kapolo woipayo anganene mumtima mwake kuti, ‘Mbuye wanga wachedwa.j]kudza kwace,’ 49 nayamba kumenya akapolo anzake, ndi kudya ndi kumwa pamodzi ndi oledzera, 50 mbuye wa kapoloyo adzafika tsiku limene iye sakumuyembekezera iye, ndi pa ola limene iye sakulidziwa. 51 Ndipo adzamdula pakati, nadzampatsa gawo lake pamodzi ndi wonyengawo. kumeneko kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.

The Man of Lawlessness

2 Concerning the coming of our Lord Jesus Christ and our being gathered to him, we ask you, brothers and sisters, 2 not to become easily unsettled or alarmed by the teaching allegedly from us—whether by a prophecy or by word of mouth or by letter—asserting that the day of the Lord has already come. 3 Don’t let anyone deceive you in any way, for that day will not come until the rebellion occurs and the man of lawlessness is revealed,  the man doomed to destruction. 4 He will oppose and will exalt himself over everything that is called God or is worshiped, so that he sets himself up in God’s temple, proclaiming himself to be God.

The Coming of the Lord

13 But we do not want you to be uninformed, brothers, about those who are asleep, that you may not grieve as others do who have no hope. 14 For since we believe that Jesus died and rose again, even so, through Jesus, God will bring with him those who have fallen asleep. 15 For this we declare to you by a word from the Lord,d that we who are alive, who are left until the coming of the Lord, will not precede those who have fallen asleep. 16 For the Lord himself will descend from heaven with a cry of command, with the voice of an archangel, and with the sound of the trumpet of God. And the dead in Christ will rise first. 17Then we who are alive, who are left, will be caught up together with them in the clouds to meet the Lord in the air, and so

in a moment, in the twinkling of an eye,
at the last trumpet; for the trumpet will sound, and the dead will be raised imperishable, and we will be changed.1 Corinthians 15:52 At the last Trumpets the Seventh trumpet. on the east of Trumpets

Matthew 24:1–51

Jesus Foretells Destruction of the Temple

24 Jesus left the temple and was going away when his disciples came to point out to him the buildings of the temple. 2 But he answered them, “You see all these, do you not? Truly, I say to you, there will not be left here one stone upon another that will not be thrown down.”

Signs of the End of the Age

3 As he sat on the Mount of Olives, the disciples came to him privately, saying, “Tell us, when will these things be, and what will be the sign of your coming and of the end of the age?” 4 And Jesus answered them, a“See that no one leads you astray. 5 For many will come in my name, saying, ‘I am the Christ,’ and they will lead many astray. 6 And you will hear of wars and rumors of wars. See that you dare not be alarmed, for this must take place, but the end is not yet. 7 For nation will rise against nation, and kingdom against kingdom, and there will be famines and earthquakes in various places. 8 All these are but the beginning of the birth pains.

9 “Then they will deliver you up to tribulation and put you to death, and you will be hated by all nations for my name’s sake. 10 And then many will fall away1 and betray one another and hate one another. 11 And many false prophets will arise and lead many astray. 12 And because lawlessness will be increased, the love of many will grow cold. 13 But the one who endures to the end will be saved. 14 And this gospel of the kingdom

15 “So when you see the abomination of desolation spoken of by the prophet Daniel, standing in the holy place (let the reader understand), 16 then let those who are in Judea flee to the mountains. 17 Let the one who is on the housetop not go down to take what is in his house, 18 and let the one who is in the field not turn back to take his cloak. 19 And balas for women who are pregnant and for those who are nursing infants in those days! 20 Pray that your flight may not be in winter or on a Sabbath. 21 For then there will be great tribulation, such as has not been from the beginning of the world until now, no, and never will be. 22 And if those days had not been cut short, no human being would be saved. But for the sake of the elect, those days will be cut short. 23 then if anyone says to you, ‘Look, here is the Christ!’ or ‘There he is!’ do not believe it. 24 For false Christs and false prophets will arise and perform great signs and wonders, so as to lead astray, if possible, even the elect. 25 See, I have told you beforehand. 26 So, if they say to you, ‘Look, he is in the wilderness,’ do not go out. If they say, ‘Look, he is in the inner rooms,’ do not believe it. 27 For as the lightning comes from the east and shines as far as the west, so will be the coming of the Son of Man. 28 Wherever the corpse is, there the vultures will gather.
 

The Coming of the Son of Man

29 “Immediately after the tribulation of those days the sun will be darkened, and the moon will not give its light, and the stars will fall from heaven, and the powers of the heavens will be shaken. 30 Then will appear in heaven the sign of the Son of Man, and then tall the tribes of the earth will mourn, and they will see the Son of Man coming on the clouds of heaven with power and great glory. 31 And we will send out his angels with a loud trumpet call, and they will gather his elect from the four winds, from one end of heaven to the other.
 

The Man of Lawlessness

2 Concerning the coming of our Lord Jesus Christ and our being gathered to him, we ask you, brothers and sisters, 2 not to become easily unsettled or alarmed by the teaching allegedly from us—whether by a prophecy or by word of mouth or by letter—asserting that the day of the Lord has already come. 3 Don’t let anyone deceive you in any way, for that day will not come until the rebellion occurs and the man of lawlessness is revealed,  the man doomed to destruction. 4 He will oppose and will exalt himself over everything that is called God or is worshiped, so that he sets himself up in God’s temple, proclaiming himself to be God.

“Immediately after the tribulation of those days the sun will be darkened, and the moon will not give its light; the stars will fall from heaven, and the powers of the heavens will be shaken. 30 Then the sign of the Son of Man will appear in heaven, and then all the tribes of the earth will mourn, and they will see the Son of Man coming on the clouds of heaven with power and great glory. 31 And He will send His angels with a great sound of a trumpet, and they will gather together His [d]elect from the four winds, from one end of heaven to the other.
bottom of page