
Kupanda Kukayikira Koyenera
Last Supper
Language
The one who belongs listens and responds to Yehovah's words. If you don't listen and respond,
it is because you don't belong to Yehovah." John 8:47
God Is Watching and listening
1 Timothy 2:12 is the twelfth verse of the second chapter of the First Epistle to Timothy. It is often quoted using the King James Version translation: But I suffer not a woman to teach, nor to usurp authority over the man, but to be in silence.
Mulungu Akuyang’ana ndipo Akumvetsera
Kuyankha » Aliyense adzakhala akudziwerengera yekha kwa Mulungu
Ahebri 9:27 Ndipo monga munthu aliyense kwaikidwiratu kufa kamodzi, ndipo pambuyo pake padzakhala chiweruzo;
Yohane 3:13Palibe munthu analowa kumwamba, koma iye amene anachokera kumwamba- Mwana wa Munthu. Machitidwe 2:29 “Anthu inu Aisraeli, ndikukuuzani motsimikiza kuti kholo lakale Davide anamwalira ndipo anaikidwa m’manda, ndipo manda ake alipo mpaka lero.” Mateyu 12:36-37 “Koma ndinena kwa inu, kuti mawu onse opanda pake amene anthu amalankhula. adzaiwerengera pa tsiku lachiweruzo. “Pakuti ndi mawu anu mudzayesedwa wolungama, ndipo ndi mawu anu mudzatsutsidwa. Machitidwe a Atumwi 17:30 “Chifukwa chake polekerera nthawi zachimbuli, Mulungu tsopano akulalikira kwa anthu, kuti anthu ponse ponse atembenuke mtima.” Aroma 14:12 Chotero aliyense wa ife adzadziŵerengera mlandu wake kwa Mulungu.
Yakobo 4:17Chifukwa chake kwa iye amene adziwa kuchita zabwino, koma osazichita, kwa iye kuli tchimo.EZEKIELE 3:2 “Komanso, munthu wolungama akatembenuka kusiya chilungamo chake, nakachita chosalungama, ndi kuika chopinga pamaso pake, adzafa; popeza sunamchenjeza iye, adzafa m’tchimo lake ndi ntchito zake zolungama. chimene anachita sichidzakumbukiridwa, koma mwazi wake ndidzaufuna pa dzanja lako.” ( Salmo 32:8 ) Ndidzakulangiza ndi kuphunzitsa iwe za njira ukayendayo, ndidzakupangira ndi diso langa lakuyang’ana iwe.
Salmo 33:18 Taonani, diso la Yehova lili pa iwo akumuopa Iye, pa iwo akuyembekeza chifundo chake; makutu amva kulira kwawo. Miyambo 28:9 Mulungu amanyansidwa ndi mapemphero a munthu amene amanyalanyaza lamulo. MIYAMBO 15:2 Lilime la anzeru lizindikira chidziwitso; koma m'kamwa mwa opusa mutulutsa utsiru. 3 Maso a Yehova ali ponseponse, napenya oipa ndi abwino. 4 Lilime lokhazika mtima pansi ndilo mtengo wa moyo, koma lilime lokhota liphwanya mzimu… Chivumbulutso 20: Ndipo ndinaona akufa, akulu ndi ang’ono, alikuyimirira kumpando wachifumu, ndipo mabuku anatsegulidwa; ndi bukhu lina linatsegulidwa, ndilo la moyo; ndipo akufa anaweruzidwa mwa zolembedwa m’mabuku, monga mwa ntchito zao. Ahebri 11:6 Ndipo wopanda chikhulupiriro sikutheka kumkondweretsa; pakuti iye wakudza kwa Mulungu ayenera kukhulupirira kuti alipo, ndi kuti ali wobwezera mphotho iwo akumfuna Iye.




